FaySam - Wabwino
Name of album : Singles Genre :Gospel
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | MobileNdi wabwino Yesu ndi wabwino Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Ndi wabwino anzanga ndi wabwino Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Pakuti onse anachimwa napelewera pamaso pa Yehova Panalibe njira ina Koma nsembe imene oyenera anali Yesu yekha Mwana wa Mílungu osalakwa Kudzafera machimo a iwe ndine míbale Kuti tikhale nawo moyo Wosatha, lelo tikutchedwa ana a Yesu Christu wa moyo Lelo ndi kunthawi zonse... Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Ndi wabwino anzanga ndi wabwino Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Dziko la Malawi, limene sitinasankhe kubadwiramo Koma munatidziwa tisanabadwe munatilenga modabwitsa Ndife odala Kukhala ndi moyo ndi chisomo Kupezeka mítsiku la lero Abale anansi abwino Mulungu mumatikondera Chikonzero chanu chabwino Ndichopambana Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Ndi wabwino anzanga ndi wabwino Ndi wabwino Yesu ndi wabwino