1694Downloads
Alinafe Jimu - Bebie Upitilize
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Bebie upitirize
Intro:
Ndi Alinafe e! Jimu bebie ndikuti upitireze, upitireze kundikonda.
VERSE ONE
Tachoka kutali iwe, tapanga chibwenzi mokwanira
Tazemeberana bebie. Sono lero ndikufuna kuti,
Tingomanga oyera, aliyense adziwe.
Kuyambira pa chibwezi, sinaone vutto lina lililonse kwaa iwe,
Chako chinali chikondi. Koma poti achikondi ambiri,
Amayamba bwino chonchi, koma sapitiriza.
Ndichifukwa chake ngakhale chikondi sapempha,
Ndikupempha upitirize, usalekelere panjira bebie.
Bebie! Bebie!
Chorus
Bebie upitirize x2
Upitirize kundikonda.
Sweet upitirize, ladie upitirize! Upitirize kundikonda.
Bebiee! X2 upitirize kundikonda.
VERSE TWO
Analiponso wena dzana, anayamba ndichikondi koma sanapitirize.
Ambiri amango kondana pachi bwenzi pokha, kumamasukirana kumayenda shosholo,
Akakwtirana mumv agawanapo zida.
Pamene tikugwirizana dziwa alipo ena, ofuna tidane azitiseka,
Chonde usawapatse m’pata.
Zomwe nkuchita m’paka mubanja ndzaona chikondi changa
Sichidzasintha. Bebie! X2
Chorus