Jungle Jex - Mantha (Jack Jones & Dre Beats)
Name of album : Mantha Genre :Afro-Dancehall
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile

Intro
Nah! Nah! Nah! Nah! Nah!
Stah! Tah! Tah! Tah! Tah!
Jungle Jex You knoooow!!
Msuli! Msuli!

VERSE 1
Akutino ndagwera ineyo,
Sizikuyenera kukhala motere//
Mu m'mbale ya zoba ngati ine,
Sukuyera kutsiramo m'mchere//
Anthu akuyankhula kwathuku//
Ndikuyenera kugwidwa ndi wa dhuku//
Ati ndiwe mkazi wa uptown//
Sukuyera kugwidwa ndi wa downtown//
Zimandipatsa ine pressure//
Polingalira mwina ndidzabetsa//
Zikundipatsa ine nkhawa//
Polingalira Kuti mwina udzanthawa//
Mapiko ndilibe ine baby Kodi sudzandisiya iwe m'malere?//
Moti utha kusankha inebe ngakhale tipangetu mayele?//
Mapiko ndilibe ine baby Kodi sudzandisiya iwe m'malere?//
Moti utha kusankha inebe ngakhale tipangetu mayele?//

HOOK
Mwina udzandinthawa..
Ayiiiiiiiiiiiih!
Mwina udzandisiya..
Ayiiiiiiiiiiiih!
Mwina udzanditaya..
Ndimangochita Mantha..
Mwina udzanditsika..
Ayiiiiiiiiiiiih!!
Mwina udzabanduka..
Ayiiiiiiiiiiiih!!
Mwina udzandileka ineyo ndimangochita Mantha..

VERSE 2
Koma beib tikakumana iweyo umatsimikiza//
Kuti ine ndisade nkhawa chifukwa umandikondera//
Moti udzandisunga//
Moti udzakhalabe//
Moti sudzatopa//
Ndisamachite Mantha//
Koma hun tikakumana umandiika pa easy//
Kuti Moto wako ndiwanga basi amuna ena sangapalize//
Mapiko ndilibe ine baby Kodi sudzandisiya iwe m'malere?//
Moti utha kusankha inebe ngakhale tipangetu mayele?//
Mapiko ndilibe ine baby Kodi sudzandisiya iwe m'malere?//
Moti utha kusankha inebe ngakhale tipangetu mayele?//

Back to Hook

Bridge
Nah Nah Nah Nah
Stah tah tah tah
Oh oh oh oh oh oh
Yeah..
Ndimachita mantha ine..
Ndimagwidwa nyetsi ine..
Ndimachita mantha ine..
Ndimagwidwa nyetsi ine..