Jungle Jex - Msamaliya ft Wikise (Prod. Jk Warrior & Dre)
Name of album : Msamaliya Genre :Dancehall
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Intro

Mmmh mmmh mmmmh mmmmh
Che Wikise Baba!!
Wakumana ndi munthu wa ambuye....

Nah Nah Nah Nah Nahyi!
Stah stah Stah Stah Stahtahyi!!

Jungle Jex You Know...

Verse 1

Wakumana ndi anyani ambiri, ena ongofuna chipatso chapakati//
Osewo amuna ausilu,amkakuona kodi kutchipa pati//
Panopa ndi man of God//
Omanya kuchenja mastyle//
Kuchezakuchezakucheza kenako kumenya masalimo//
Mbiri ndainva kumene ukuchoka//
Unangogiver ukuku ndikutopa//
Mbiri ndainva ndabwera ndifufute//
Chikondi chako usati uchifutse//
Hook

Lero ndi lero ndi lero
Chikondi chija uchinveno kukoma//
Lero ndi lero ndi lero
Chikondi chija uchinveno kusintha//
Wakumana ndi munthu wa Mulungu.
Chikondi chija uchinveno kukokoma//
Wakumana ndi munthu wa Ambuye
Chikondi chija uchinveno kusintha//
Verse 2

Osakhala ndi mtima odhauta//
Wakutengayu ndi munthu wachautu//
Ndipo iweyotu uli monyawuda//
Ndiwe ogwidwa udziyankha mwa louder//
Chikondi changa changa ndichodalitsika//
Wakumwambayo kale adachitsilika//
Kusintha kusintha kwadzano//
Ngati kunali m'dima pano titi kwachano//
Mbiri ndainva wafika pongotopatopa//
Ndi chikondi chamadobadoba//
Sindikukana wafika pongofookafooka//
Ndi chikondi chamafoshafosha//
Verse 3

Wikise
Beib i can see
Unakondedwapo ndi achina yudasi
Ankangokuzuza dairy kukhalira mambazi
But Dont worry
Mavuto ako onse atha
Ndine wako mesiya
Muyaya sinzakusiya
Bwera uchilawe chamkachisi
Cha abusa chikondi
Chama libakateliya malipapakakatala