134310Downloads
Saint - Delilah
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Timano tako ukamasekelera
Timau tako ukamandiyandkhula
Timaso tako ukandiyang'ana,, ndimafa head
Timiyendo tako ukaponya step
Kambina kako mkumagwedezera
Timanja tako tikandikhudza
ndimadzifunsa aah..
kuti,,,
Pre chorus;
Sudzandidyera chuma changa iwe
Delilah
Sudzawazunza abale anga iwe
Delilah
Mkundipereka kwa adani
Ngati Delilah..*2
Chorus;;
Delilah ah ah aaah
Unene eeh eh
Delilah ah ah aaah
Unene eh eh
Delilah eeh eh
Unene eh eh
Ndidziwe Delilah *2
Verse 2
Mwina umphawi wanga siudzatha chifukwa cha iwe
Abale ndi amzanga mkudzadana chifukwa cha iwe
Mwina udzandiika pampeni, kwa adani anga nena zeni zeni
Iwe, siwe woyendayenda ngati enawa/
Sudzanditengera matenda mkundithawa ine
Ndimapemphera// kodi mkubwera kwako simdzasochera ine?
Mbuye adandidalitsa kodi mkubwera kwako sanditembelera ine?
ndidziwe, kapena mwina ntchito mkudzatha
Kapena mwina mdzayamba ine kupita...
kumanda mtakusiya ndi ana,
unene kodi udzawasamala.
BACK TO THE PRE CHORUS
BACK TO THE MAIN CHORUS
Bridge ;;
Delilah ah, simfuna kudzalira aah
Ngati Samson,ngati samson
I say Delilah
Sindikukaikila aaah
koma ngati samson, simfuna kudzalira aaaah