39Downloads
Phyzix - Never Be Alone ft Ruth Kulaisi & Aliyssa Grace

Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Song: *NEVER BE ALONE*
Artists: *Phyzix, Ruth Kulaisi, Alyssa Grace*
Producers: *Ace Tee Beats, Tricky Beatz, Stich Fray*
Label: *It’s Only Entertainment (IOE)*
Songwriters: *Noel Chikoleka, Ruth Kulaisi-Chikoleka, Alyssa Grace Chikoleka*
Release Date: *August 2025*
Genre: *Hip Hop/Soul*
*(INTRO: Phyzix, Ruth Kulaisi, Alyssa Grace)*
This one for Alyssa
(Ace Tee on the beat)
Mmmmmmmmh
For Alyssa
This one for Alyssa
You can never be alone
Phyzix (My baby)
Ruth
You can never be alone
Captain Bae
Mmmmmmmmh
Very Good (Very Good)
*(VERSE 1: Phyzix)*
Ulemu wako mwana wa mkazi/ Ndimadziwa umakumana ndi zambiri (ndi zambiri)
Amakuzunza mopanda manyazi/ umapempherabe mbuye awakhululukire (awakhululukire)
Unabadwa bwanji kulimba chonchi/ zokupinga ndi zambiri kuposa tsitsi (eh?)
Ukuyenera kuziphoda/ sungatuluke pa gate osapesa tsitsi
Ukuyenera kudzi holder/ kukanika kupanga zomwe mtima ukufuna
Oyenera kukuteteza/ ndi omwe akuyamba kukupweteka (mmh)
Oyenera kukukonda/ ndi omwe akuyamba kukugenda (mmmh)
Sizingatheke kuti uzakhale wekha/ zokanika munthu amazitha Namalenga
*(CHORUS: Ruth Kulaisi, Phyzix)*
You can Never be alone/ You can never be alone my baby (x2)
Nzosatheka kukhala wekha/ Ingodekha mmmh my baby
You can Never be alone
You can never be alone my baby
*(VERSE 2: Phyzix)*
Unabadwa ndi nzeru osaopa kulimbika kuti umposa mwamuna wako (mmh)
Unabadwa okongola sikuti unamulola ndekuti aononge nkhope yako (no baby)
Usamakanike kugona baby
Kuti mawa dzuwa siliwala maybe
Usadzasiye kusekelera/ Alipo ambiri okupemphelera (Amen)
Oyenera kukuteteza/ ndi omwe akuyamba kukupweteka (my baby) (mmmh)
Oyenera kukukonda/ ndi omwe akuyamba kukugenda (my baby) (mmmh)
Sizingatheke kuti uzakhale wekha/ zokanika munthu amazitha Namalenga (x2)
*(BRIDGE: Ruth Kulaisi)*
You can Never be alone. You can never be alone my baby (x4)
*(CHORUS: Ruth Kulaisi, Phyzix)*
You can Never be alone. You can never be alone my baby (x4)
Nzosatheka kukhala wekha/ Ingodekha mmmh my baby (x3)
You can Never be alone. You can never be alone my baby
*(OUTRO: Alyssa Grace, Ruth Kulaisi)*
Nzosatheka kukhala wekha/ Ingodekha mmmh my baby (x3)