12566Downloads
Phyzix - Wena (Prod. by BFB x Tricky Beatz)
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Man Phyzo
Gamba
Cholapitsa
Captain Bae
Very good, very good, very good
HOOK
Am the King of the Ghetto (Wena)
Osamaphweketsa deal (Wena)
Ndinamva kale kuwawa (Wena)
Iweso ndiwe kandani? (Wena)
Captain Captain Captain Captain Bae Bae Bae
Kunyetsa mafana nonse mumva M'bebebe X2
VERSE 1
Ndimalamulira Ghetto Kingdom|
Ana enawa ndima ghetto fong kong|
Ndimaika mtima onse on a song|
Mafanawa ana riser when I was gone|
I'm back on the throne, I'm the KING here|
Ndiwe mwana sungandipose, am sincere|
Cholapitsa chikulapitsa your sins here|
As a matter of fact your career ends here|
Unalowa kolakwika, reverse gear|
Mgodiwu ndiwaineyo ndine ojiya|
Ndiyambano kucharger zomangotchula ghetto¦
Mwadyera kokwana dzina la ghetto pano mapeto|
HOOK
Am the King of the Ghetto (Wena)
Osamaphweketsa deal (Wena)
Ndinamva kale kuwawa (Wena)
Iweso ndiwe kandani? (Wena)
Captain Captain Captain Captain Bae Bae Bae
Kunyetsa mafana nonse mumva M'bebebe X2
VERSE 2
Am here to restore things back to order¦
Better prepare it's gonna be a long summer¦
I have never been alive like this¦
You can't touch this but am no Hammer
Unapita kukandinyoza pa radio¦
Kutchula dzina la makolo anga mu nyimbo|
Mpingo, timutani mfanayu?|
Sakudziwa ndine oblowa kuposa how are you?¦
Ndimakupilira chifukwa okulipira|
Ndiyemweyeso ineyo amandilipira|
Nde kochokera dollar sitimatseka njira|
Poti panopa unachokako, ndikukhiya¦
HOOK
Am the King of the Ghetto (Wena)
Osamaphweketsa deal (Wena)
Ndinamva kale kuwawa (Wena)
Iweso ndiwe kandani? (Wena)
Captain Captain Captain Captain Bae Bae Bae
Kunyetsa mafana nonse mumva M'bebebe X2