32151Downloads
Battafly - Unali Kuti

Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Ndazindikira ine kuti chikondi ndichokoma
Akazi onse m’mbuyomu amkangondi user
I regret now
CHORUSUmachedwa kuti iwe
M’mbuyo monsemu_ena amkangondiseweletsa mtima
Unali kuti iwe
Nthawi yonseyi_ndimkasowa chikondi chako
Umachedwa kuti iwe
M’mbuyo monsemu_ena amkangondiseweletsa mtima
Unali kuti iwe
Nthawi yonseyi_ndimkasowa chikondi chako
VERSE ONENdinafika pongovomeleza ndikumati
True love never exist
Nanga chikondi chomwechi
Wina akunjoya wina akumvetsedwa kuwawa
Koma kubwera kwako mmoyo mwanga
Kwandipangitsa_ndilimbenso mtima
Koma kundikonda kwako iwe
Kwandipangitsa ndichidzidziwe chikondi
CHORUS
VERSE TWO
Kukonda ndimkakonda koma kukonda olakwika
Ndimkayesetsa koma zimkangovuta
Pena umakhala kapolo wachikondi
Kumamukonda koma osakondedwa
Gal u came in my life with a posibility
Wangobwera m’moyo mwanga chilichonse kusintha
Ndi iwe ndalimbanso mtima
Kukonda kwako pano ndikukamba zina
BRIDGE
One thing I know about love
Chikondi sichitengera experience
Chikondi ndimumtima take it easy osapnga phuma
BACK TO CHORUS
VERSE THREE
Wandionetsa kuwala chikondi chako chili ngati makhwala a moyo wanga
Iwe mkazi unafatsa you amaze me ndichikondi umandipatsa m’moyo mwanga ah ey
(ndichikondi umandipatsa m’moyo mwanga ah eey)