5100Downloads
Phyzix - Sudziwa Ft Quest (Prod. Jay Mass & Ace Tee Beats)

Click here to download this song >> Desktop | Mobile
(INTRO: Quest)
{Dziwa}
Oh ohhhhh
Ace-Tee on the beats
{Dziwa}
{aaaah aah}
{Dziwa}
It’s Only Entertainment
Oh ohhhhh
{Dziwa}
Mmhuh
(CHORUS: Quest)
Kuona maso a nkhono nkudekha
{Dekha Dekha Dekha Dekha}
Kusamala moyoso nde ndiwekha
Kukonda munthu ndi wekha
Koma osaiwala kumazikonda wekha
Poti chobwela mawa
Sudziwa/ sudziwa
Sudziwa/ sudziwa
Sudziwa/ sudziwa
Sudziwa/ sudziwa
(VERSE 1: Phyzix)
Anali mnzanga koma pano tinadana/ wachikondi wanga uja sitityakhulitsana/ Ena tinadana chifukwa cha mtsikana/ ena kukula mtima basi ku sizer'na/ Zambirimbiri zimatiphinja talking about it brings relief/ zanga ndimaziika munyimbo brother that's my release/ kusaka ndalama but really searching for peace/ wanna make clean money ndisamathawe Police/ ungadziwe tsiku lomaliiza ndi liti?/ awa ndi Akhristu kapena afiti?/ akatisunga kapena amakonda ma skirt?/ banja ndikupilira kapena mpange quit?
(CHORUS: Quest)
Kuona maso a nkhono nkudekha
{Dekha Dekha Dekha Dekha}
Kusamala moyoso nde ndiwekha
Kukonda munthu ndi wekha
Koma osaiwala kumazikonda wekha
Poti chobwela mawa
Sudziwa/ sudziwa
Sudziwa/ sudziwa
Sudziwa/ sudziwa
Sudziwa/ sudziwa
(VERSE 2: Phyzix)
Sitimadziwa tsiku lolemera olo losauka/ sitimadziwa kuti tikagona mawa tiuka?/ Kunjaku kukacha tiipeza ya Ufa?/ Kodi ndi chikondi kapena kapena akutiuser?/ Mumazipeza bwanji pamene ife tuzisowa/ sitimatchuka koma nafenso tili ndi malusowa/ kalikonseko m'nakaona mboni ndi masowa/ kalikonseko m'nayesapo osapeza cholowa/ poti za mawa sudziwa sudziwa/ utha kumavala ma suit wa suit wa/ kenako mawa uli ndi usiwa ndi usiwa/ chinyumba chabwino kusanduka siwa/ yeah
(CHORUS: Quest)
Kuona maso a nkhono nkudekha
{Dekha Dekha Dekha Dekha}
Kusamala moyoso nde ndiwekha
Kukonda munthu ndi wekha
Koma osaiwala kumazikonda wekha
Poti chobwela mawa
Sudziwa/ sudziwa
Sudziwa/ sudziwa
Sudziwa/ sudziwa
Sudziwa/ sudziwa
(OUTRO: Phyzix & Quest)
{Sudziwa aaaah}
Phyzix
{Sudziwa aah ah}
Quest
{Sudziwa aaaah}
Yeah
{Sudziwa aah ah}
Very Good Very Good