Piksy - Unamata
Name of album : Maso Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


 


VERSE ONE


Kumata kumata ndi superglue


Uli duu


Kuutolatola mtima wanga pansi uli mbuu


Kumata ndi bostic


Mbali zonse kuchta stick


2getha wambawamba osamvetsa yako logic


Unali wanga driver


So loyal to me sunasamale nkhan zomwe unazimva


Kundimatilira maso ako pa future


Kunali chi mdima koma unkadziwa kucha.


Kundisekerera


Nkamazima kupemelera


Moyenera


Kundinyengelera mpaka ntakolera


Sizinkabisika nanenso ndinkahopela


Koma kugwa muchkondi simmene ndinkaopela.


Ngati kabebe unandilera.


Ikamagwa mvula unali umblera.


Zomwe unamatazi sizingatheke kumatula.


Chikondi chako ndalama sizingathe kugula.


CHORUS


Unatola mtima wanga uli wosweka, ulibe mantha


Mmene ena anaseka, nati ndatheka unanditsata


Unamata-mata-mata-mata-mata-mata mtima wanga


Mtima wanga unawina


Sindingampatse wina


VERSE TWO


Yako fandum


Ngat yochita kupanga zoom


Ndikondwa mudzi  wako onseu ndine mfumu


Unamatamatako konse sunasiye room


Ena kumayesera kuti alowe koma hmmm?


Ndimakondwera  ndikamaona ka view.


Nde iweyo ameneyo everyday u look brand new


Ndichikondi chako chomwe chindipatsa mphamvu


Zonsezi in one sentence honey i love you


Kukusiya iwe ndikuluza timing


Poti munyengo yaziphaliwali u stood by me


In so doing unawina chikondi cha ine


Mpaka muyaya ndiri nawe n'patse poti nsaine.


Unakhulupira mwa ine kuchoka pa chyambi


Ndisanapsetsetse ndikumveka khambi.


Pano ndapsano umveno ku-kukoma kwa changachi


chikondi


udzingopanga download.


VERSE THREE


Mu mvula ya ziphaliwaliwali unandikonda more


Kumangofeela warm – kumangofeela bho


Kuthamangitsa zinthu zanga zikamayenda slow


Kumangofeela bho – kumangofeela bho


Si inenso wamanyazi sweetie you make me stand tall


Kumangofeela bho – ine kumangofeela bho


Usiku usanagone kundimenyera ka call


Kumangofeela bho – kumangofeela bho