Phyzix - Cholapitsa 2.0 ft Oath
Name of album : Cholapitsa 2.0 Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


CHOLAPITSA 2.0 Lyrics by Phyzix & Oath

(INTRO: Phyzix)
Yeah
It’s Only Entertainment
Yeah
Very Good Very Good
Atigo/ Phyzix/ Atigo/ Atigooooooo
Yeah Yeah Yeah

(VERSE 1: Phyzix)
Chenicheni cha kumudzi chi mfana/ mcha ku 25 sichinama/ cholapitsa kuchokera pobadwa/ amachitcha Phyzo Phyzix/ chimakuwa ngati mfana wotchukuma/ ndichomyata chilibe phuma/ ndichibavu ukachiputa chikuluma/ chimayenda opanda nsapato/ muchifumbi cha kwawo ku 25/ sizichikhudza bola chili moyo/ sichimunthu anzanga mchingamunthu/ pa daily paja chimakhalira pa nsenga/ kumwa kanthu kalikonse molapitsa/ kusanza kalikonse ndi matumbo omwe/ sichimunthu magaye mchigandanga/ nchonyasa nchosasa mau/ mcha afro chimavala boxer wa umbro/ ndipo chimanunkha bwemba/ nchosasowa ndi chachitali/ chimawala patali wali wali/

(HOOK: Phyzix & Oath)
Ndikumyatitsa mfana umyata
Ndikumyatitsa mfana umyata
Umanama ndine Cholapitsa
Umyata mfana umyata
Ndikumyatitsa mfana umyata
Ndikumyatitsa mfana umyata
Umanama ndine Cholapitsa
Umyata mfana umyata

(VERSE 2: Phyzix)
Cinderella night club is where you find me/ on a Friday night son we wildin’/ wit’ my boy/ John Chikheba/ kumwa kalikonse molapitsa/ from Green to Stout to Zinyama zolusa/ ndamwa kanthu tsopano nditokote/ drunken master tactics tsano/ ndi momwe ndikuchezera masiku ano/ ndinasiya za chibwana no mano/ kumyatitsa aliyense wa mwano/ ndachokera kutali zedi mfana/ I been in the underground like a cockroach/ like a rat m’mandiponyela Temik/ m’malo mofa ndikubwera mwa revenge/ I’m coming for your neck son I’ma bite ya/ stay away from this mean Emcee (MC)/ you can’t match with these furious forces/ I’m the Phyzix and I’m disastrous/ ukuchepa mfana ukuchepa/ ukuchepa mfana ukuchepa

(HOOK: Phyzix & Oath)
Ndikumyatitsa mfana umyata
Ndikumyatitsa mfana umyata
Umanama ndine Cholapitsa
Umyata mfana umyata
Ndikumyatitsa mfana umyata
Ndikumyatitsa mfana umyata
Umanama ndine Cholapitsa
Umyata mfana umyata

(VERSE 3: Phyzix)
Ndatopa nanu inu anthu ondisaka/ simunditha ndine Cholapitsa/ you can’t see/ I’m steady like chitsa/ stop that usanyasitse nkhope/ ndikumwetsa mutu wa kachasu mfana/ jang’ala bibida ndimamwa/ ndine nyau pedegu ndi ine/ kang’wing’wi chadzunda ndi ine/ mukunena nena nena ma lilime/ mkumangoomba makoma ngati mileme/ musadadwe/ ndine ndemwe/ Phyzix on the mic son I’m that nice/

(BRIDGE: Phyzix & Oath)
Cholapitsa/ cholapitsa/ cholapitsa ndine cholapitsa/ Cholapitsa/ cholapitsa/ cholapitsa ndine cholapitsa

(CHORUS: Phyzix & Oath)
Siya za matukutuku ndiwe mfana
Siunditha ndine Cholapitsa
Umyata mfana umyata
Umyata mfana umyata
Siya za matukutuku ndiwe mfana
Siunditha ndine Cholapitsa
Umyata mfana umyata
Umyata mfana umyata