60359Downloads
NesNes - Mlendo
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Kumapita no
Sinabwele kuzacheza kumapita
Ine kumapita no
Kapena kuzangowona kumapita
Ine kumapita no
Ndabwela kuzakhazikika moyo
Mwako lady
Chorus
Usakayike eee sine mlendo
Moyo mwako bady sindichoka eee
Usakayike eee sine mlendo ndikhazikika bady
Sindichoka oh oh oh oh oh
Verse 2
Sinabwele kuzapanga masewela
Masewela no
Kapena kuzakhumudwitsa mtima wako
Mtima wako oh no
Sindifuna kungodusa kumapita
Ine kumapita no
Ndabwela kuzakhazikika mdziko lako oh ooh
Verse 3
Uuuuu oh oh oh oh nesnes
Sinabwele kuzangodya kumapita
Kumapita no
Sinabwele kuzacheza kumapita
Ine kumapia no
Kapena kuzangowona kumapita
Ine kumapita no
Ndabwela kuzakhazikika moyo
Mwako lady