Excess - Zima Wa Wawa
Name of album : EXCESS VS EKISESI Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


EKISESI ft EXCESS-ZIMAWAWAWA

Zikamayenda
Akaona tikuchita bwino
Akaona tikulimbikilaaaa iwooo
Zimawawawa yeahhhh


Verse 1 EKISESI
Amafuna zawo zokha ziziyenda
Akaona nawe ukuchita bwino amakujeda
Ukakhala ukuwaposa mtima saupeza
Akaona ukupita amabwela kukubwenza
Pamwamba wayimapo akufuna atakugwetsa
Sakuonela kukondwa ndi afiti opemphela 
Ukayang’ana kumbali azabwela kukutchetcha
Moto wako ukamazima sadzafuna kupemelela
Anthu ena sungawamvetse ali ndi mtima wansanje
Amafuna zonse zikhale zawo, mzawo zisafwambe
Ukavutika uwawona iwo ali m’ma happy
Pamene wakondwela iwo sangasangalale

Verse 2 EXCESS
To them life, is all about the competitions
They never like it when they see you on the top positions
They wanna be you but cant, they hate without a reason
Yaol can never be successful, yaol stuck in that envy prison
You have you own world, your own belief, your own religion
I see you’re about living life without a vision
Hating on us is like burning grass in rainy season
Forget your old ways, its time to switch to new editions
This goes to people that only see all the wrong you do
They never congratulate but criticize your every move
Jealousy is drivin em, they only envy you
All that gossip and hating are really never worth it dude

VERSE 3
Ekisesi
Tsopano mvela langizo limene nditakupatse
Mzako zikamayenda, khale phee zisakunyase
Musamufunile zoyipa koma zaubwino
Kulimbana ndimunthu popanda chifukwa ndi uchimo
Excess
Really it is a sin, for real it is a sin!
Instead of holding hands they’re all about who is to win
Ekisesi
Zako zikayela azabwela azidetse
Zomwe amachita anthuwa ndithu sungazimvetse