Piksy - 40 (Forty)
Name of album : 40 Genre :Afro-Pop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Verse one

Anthu ena ndi dzilombo,
Ukangoiphula mpamene waputa nkhondo
Ayiwala nawo ndi dongo
Atamenya hustle nawo angafike pompo
Alimbikira kumenya maupo
kubindikira kukupempherera down fall
Ayiwala mulungu si munthu awa amvabe kuwawa

Bridge

Asiye athoke
Koma nje usafoke
Poti adzasintha nkhope
Likamukwanira la forty
Adzadya matope
Zidzatha dzilope
Nde adzasintha nkhope
Likamukwanira la forty

HOOK

Forty x3
Limakwana la forty
Forty x3
Lidzakwana la forty

Verse 2

Akuyuza Facebook
Kuwauza anthu ati iwe wa Duu
Ati ulibe kanthuuu
Kumenya ma comment kumaseka with fools
Kumachulutsa ma excuse
Sakugwira ntchito angokhalira booze
Munthu koma maganizo ngati mbuzi
Chifukwa chakeno they still loose


Bridge

Asiye athoke
Koma nje usafoke
Poti adzasintha nkhope
Likamukwanira la forty
Adzadya matope
Zidzatha dzilope
Nde adzasintha nkhope
Likamukwanira la forty


Hook

Forty x3
Limakwana la forty
Forty x3
Lidzakwana la forty