Clemo Tryphks - Ndilibe Chikondi
Name of album : Singles Genre :Dancehall
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | MobileINTRO Uu yeah pepani chemwali Pepani adona Chikondi ndilibe Chikondi ndisowa Ndilibe ndilibe ehy! #HOOK Pepani chemwali×2 Pepani adona×2 Chikondi ndilibe Chikondi ndisowa Chikondi ndilibe Chikondi ndisowaaa ah #VS 1 Chikondi kuchi-player Chikondi kuchiyesa Usalire poti wabetsa Usalire pot waliza Chikondi nchotani Mtima ndiotani Ndinali ofatsa odekha ,odekha,izi ndi izi ine ayi Koma leronso mwaliwe Wandifunaso bwanjiwe Ndilibe chikondiwe Ndilibenso mpata owe Chikondi ndilibe Chikondi ndisowa chikondi ndilibe Chikondi ndisowaa #HOOK HOOK HOOK #HOOK HOOK #HOOK Chemwali pepani ndithu Chikondi sima-share U need to take care Komaso kunvetsetsa Nakuuza izi leka Nasamala iwe wekha Nakuuza udzalira Iweyo udzandisowa Chikondi ndinali nacho Pa iwe anga maso Pepani ndilibe kaso Poti mtima waswekaso Chikondi ndilibe Chikondi ndisowa Chikondi ndilibe Chikondi ndisowaa #HOOK HOOK HOOK #HOOK HOOK #HOOK #BRIDGE Uu yeah pepani chemwali Pepani adona Chikondi ndilibe Chikondi ndisowa Ndilibe ndilibe ehy! #HOOK HOOK HOOK #HOOK HOOK #HOOK BAKINGZ;;;inu Inu Sortie Babie Sortie Babie

 • Malawi-Music Blog

 • ABOUT

  Through this portal, Malawi-music.com provides you with the lyrics of the top songs in Malawi.

  This is your number 1 spot for up-to-date lyrics of the latest top songs in the country

  Visit Malawi-music.com to download more songs from your favourite local artists.

  Visit the Malawi-Music Blog to get the latest news updates on what's happening in the music industry.

  And also Checkout videos.malawi-music.com to watch and download the top videos in the country.

 • Other Links

 • Malawi News

Malawi Music Lyrics by Malawi-Music.com