12477Downloads
Queen Mishu - Bae Usazafe [Prod By Chycoon & Dj Langie]
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
its a love song... its ur gal Queen mishuuu
its a love..
( Verse 1)
*Hello Bebie tabwela ndikuone eyaaaa
*ndikakhala osakuona sindinva bwino owuwoo
*chikondi chimenechi sichanormal
*mkakusowa ndimafila abnormal
*unapukuta misozi yangaa
*pano zoliraliralira normal..
*usadzafe udzangosowa eee umandinvesa kukomaa....
(Hook)
Usadzafee bae....Udzangosowaaaa
Chikondi chako,,chimandinvesa kukomaaa
Usadzafe bae,...unabwelesa chimwemwe mmoyo mwanga..
Usadzafe bae, love yako imandinvesa kukomaaaaa..
(Verse 2)
*Am so lucky to have you..your one in a million.
*Am inlove am inlove with you love yako imaposa billion..
*Ndikakhala osanvako mawu ako
*Tsiku langa limabhowaa.. *Ndinathela paiwe honey usadzafe udzangosowa.
*Ndikulonjeza sinzakuthawa,,,ndikulonjeza sinzakusiyaaaa....
(Hook)
Usadzafee bae....Udzangosowaaaa
Chikondi chako,,chimandinvesa kukomaaa
Usadzafe bae,...unabwelesa chimwemwe mmoyo mwanga..
Usadzafe bae, love yako imandinvesa kukomaaaaa..
(bridge)
Ooooooowa owowo owowooooo
Usadzafe udzangosoooooowa Bebie
Ooooooowa owowo owowooooo
Usadzafe udzangosoooooowa Bebie
Usadzafe udzangosoooooowaa Bebie
(Hook)
Usadzafee bae....Udzangosowaaaa
Chikondi chako,,chimandinvesa kukomaaa
Usadzafe bae,...unabwelesa chimwemwe mmoyo mwanga..
Usadzafe bae, love yako imandinvesa kukomaaaaa..×2