FaySam - Wabwino
Name of album : Singles Genre :Gospel
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


Ndi wabwino Yesu ndi wabwino
Ndi wabwino Yesu ndi wabwino
Ndi wabwino anzanga ndi wabwino
Ndi wabwino Yesu ndi wabwino

Pakuti onse anachimwa napelewera pamaso pa Yehova
Panalibe njira ina
Koma nsembe imene oyenera anali Yesu yekha
Mwana wa M’lungu osalakwa
Kudzafera machimo a iwe ndine m’bale
Kuti tikhale nawo moyo
Wosatha, lelo tikutchedwa ana a Yesu Christu wa moyo
Lelo ndi kunthawi zonse...

Ndi wabwino Yesu ndi wabwino
Ndi wabwino Yesu ndi wabwino
Ndi wabwino anzanga ndi wabwino
Ndi wabwino Yesu ndi wabwino

Dziko la Malawi, limene sitinasankhe kubadwiramo
Koma munatidziwa tisanabadwe munatilenga modabwitsa
Ndife odala
Kukhala ndi moyo ndi chisomo
Kupezeka m’tsiku la lero
Abale anansi abwino
Mulungu mumatikondera
Chikonzero chanu chabwino
Ndichopambana

Ndi wabwino Yesu ndi wabwino
Ndi wabwino Yesu ndi wabwino
Ndi wabwino anzanga ndi wabwino
Ndi wabwino Yesu ndi wabwino