18048Downloads
KYC Nyimbo - Mantha A Muyaya ft Eddie
Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Anayamba Masiku, Kenako Sabata/
Kenako Miyezi, Kenako Zaka/
Ma Text Apafupipafupi Aja Anatha/
Sindikudziwa Chilipobe Kapena Chinatha/
Koma sitinayambane, sitinakangane /
Sitinamenyane, sitinadane/
Chomwe ndikudziwa ndichoti sitinathane/
Koma mwina maganizo anga ndi ako sangafanane/
Ndikamakhala ndimati chibwezicho chilipo/
Ndipo relationship status ya ine siili single/
Koma alikutiko? Anzanga amandifunsa/
Ati ndingodikilira mwina wina akususa/
Ndimayesesa kuti nsapeze kena ko hitter/
Coz if i do that, i'll prolly be called a cheater/
So i dnt wanna be called names for no reason/
Ur last words Will set me free from this love prison
CHORUS - EDDIE
VERSE 2
Unayamba wakhala tsiku lina kulingalira?/
Zamasiku ambuyo ndimene tinkachitira/
And if u had a wish ungasankhe ubwelere kaye?/
Kapena zako zilibwino pano kuposa kale?/
But, truth be told ndalisowa kale lathu/
Tinali tight sitimkamva zonena za anthu/
Chibwezi chathu, chinali mkamwamkamwa mwa anthu/
Chibwezi choyamba ndichovuta kuiwala ndithu/
Distance, inasokoneza chilichonse/
For instance, mwina sungandikondeso konse/
But i hope i still runs in ur mind like a river/
Nzotheka mwina kamba ka distance unagiver/
Ndikudziwa ndiwe mkazi mayesero ndosanena/
Amuna akoso ndi celeb pano sunamve kapena?/
Nde nyimbo iliyonse imakopa ma hope ena/
Zimafunika kupewa kutseka khutu kapena
CHORUS - EDDIE