Piksy - Ponya Mwendo
Name of album : Maso Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile
PONYA  MWENDO  LYRICS


By Piksy


INTRO


Okay…intro kaye


Hmmm mmm hm hm hm hm


Koma ndikaponya beat


Ndingobwera ndi ma hit


Sikuti ndikukweza kamba mu mtengo…..ndeno..


Mhu


CHORUS *2


Koma ndikaponya beat (Ponya mwendo)


Ndingobwera ndi ma hit (Ponya mwendo)


Sikuti ndikukweza Kamba mu mtengo


Pali nyimbo palibe ulendo


VERSE ONE


P . I . K . S. Y – Piksy


Ndikudumpha dumpha  luso lisabisike


Nyengo yasintha koma sindikhala chete


Nyimbo sinkhani, ma style ndi plenty


They been doin’ bad…I been doin’ good


Angoshara mu hood


Angosuta ndudu


Ali duu ine ndikuponda ponda


Mpake pali mau woti makonda makonda


Zikuyenda palibe akutsutsa


Akudziwa kuyambana ndi Piksy ndi suicide


Tchu-tchu-tchu ndikubwera n’zen-zen


Position yanga kuichita maintain


Thupi langa lili flexible


Atsatsuna ena ati ndiri edible


Nde, ndimati nkangogwedeza chiuno


Piksy, uzibwera bwera kwathu kuno


Shaaa!


CHORUS *2


 


VERSE TWO


Ngati Third Eye…..Umajaja


Chi Piksy changotuluka mu graja


Ngati basket ball ndikunjanja


Ngakhale ndiri mtsinje ndikufeela ngati Nyanja


Fans ikandiwona chimwemwe kudzaza


Zoti iwo amandifeela nzomwe ndimayaza


Ma vendor, ma soldier ndi ma panza


Amakonda nyimbo zomwe ndimamanza


Poti ndimakana 2 andipatsa one


Ena amanditcha MC wamakani


Kuyankhula za ineyo sikusowa nkhani


Kaya zachikondi, kaya za chidani


Nthawi zina ndimafeela ngati raster


Sorry, ndimafuna nnene kuti master


Akandiwona mtima kuthawa


Inde, amandibeefa akufuna kungotchuka awa


 


CHORUS


 


VERSE THREE


Shaaa


Fans imandifeela


Mu hood ndingochilla


Ma haters angolira


Kuphika beef mitu yawo sikugwira


Sangazikolope nyumba zawo ndizozira


Ndimathoka mwa chipongwe


Ati tichite njibwa kuti Piksy agonje


Poti speaker imanditchula cousin


Microphone amanditchula darling


Nyimbo zanga ziri super kuchititsa chiwalo chirichonse kudumpha


Nyimbo zanga ziri super kuchititsa chiwalo chirichonse kupuma


Nyimbo zanga ziri super  kuchititsa chiwalo chilichonse kusuntha


 


CHORUS TILL FADE