5049Downloads
Ambokire Salimu - Timadziwana Ndi A Chilima

Click here to download this song >> Desktop | Mobile
Chorus
Aliyense azatukukila thukuta lake
Tisawasokoneze awa andale athu ×2
Verse 1
Timadziwana ndi ACHILIMA
Pano tasiyanso kulima
Timaadziwa aMtharika
Ndalama zathu zitalika
Back to Chorus
Verse 2
Ati amamudziwa Chalamanda
Amamudziwa Atupele
Amawadziwa Atcheya
Ati zao pano ziyamba kuyenda×2
Back to Chorus