Phyzix - Pa Ground ft Daredevilz (Prod. Stich Fray & Daredevillz)
Name of album : Pa Ground Genre :Hip Hop
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


(Verse 1: Phyzix)
Akubwera ndi chigulu cha mipaliro/
ndikapanga zibwana nthokhala maliro/
akufuna zake komano date yo/
ndizitenga kutiko zobweza la lero/
akuchita kukuwa kuti iwe na lero/
tikufinya finya utuluka za yellow/
ndimafuna kuthawa ati gwirani Mani yo/
akuti andiyalutsa andijambula-video/
ndizichita kuveka mau anga pa-audio/
kuti kape uja zamuthina kuno/
tachita kumutulutsa blood mphuno/
timulanda zovala ayenda buno/
aphuzire kumadya ndalama bwino/
sizikutuluka wamba Boma lino/
pa Ground sipali bho/ no malido/
panopo sitikumadya nkhomaliro/ eh

(Hook: GD)
Ndikumayenda cha mpeni/ zweee
Asandipeze pa den/ No No No
Akumabwera ndi zi mipeni/
Zi agalu atazimanga ku matcheni
Pa Ground sipali bho/ No No No
Pa Ground sipali bho/ No No No
Pa Ground sipali bho/ No No No
Pa Ground sipali bho
axe ndi black tax/ chilungamo chake panopo life sucks

(Verse 3: GD)
Bebi yanga wandilanda blesser/
sizimandiwaza zoti ngini izindi stresser/
ndikumenya goals iwe busy kupatsa pressure/
ndikumva kuwawa ngati drink yopanda chaser/
pa ground sipali bho player akungotelera/
izi ndi zenzeni awawa si masewera/
ine ndilibe kanthu ngati truck yopanda telera/
one by one ngati mwana akudya cerelac

(Verse 4: Marcus)
GD/ mabwana sakulipira/
maluzi andipha olo mkazi sakulilira/
Landlord mpaka 5 missed calls/
m’town ndilimba?/
kupanda Prophet ndi masten bwenzi ine ndili ndani/
ndadzala mitengo koma osafetsa/
simdzatenganso katapila adzandiphetsa/
mwina ndiyambe Pente ndisiye mu Mpesa/
Pa Ground ndithana napo mwazi ndiukhetsa