Cassim Ibrahim - Zindikirani
Name of album : Zindikirani Genre :Afrobeat
Thumbnail

Click here to download this song >> Desktop | Mobile


INTRO

Some Facts About Life!
Strongingo...
Hash!

*VERSE - 1

Poti Siudziwa! Kuti Mawa Kudzacha Bwanji...
Tsiku Lidzayenda Bwanji?
Poti Siudziwa Aaaa!

Poti Siudziwa!
Moyo Udzakhala Otani?
Udzakumana Ndizotani?
Poti Siudziwa Aaaa!

Poti Siudziwa!
Abale Uwanyoza lero...
Mawa Udzawakumbuka...
Poti Siudziwa Aaaa!


Poti Siudziwa!
Mwai wa Sukulu Ukuwuseweretsa ...
Mawa Udzawukumbuka...
Kodi Siudziwa?

Kodi Siudziwa,?
Wachikondi Umunyoza Lero
Mawa Sadzakhalapo ...
Kodi Siudziwa???

*#CHORUS*

Zindikirani!
Zindikirani!
Mungadzalire
Zinthu zimatha kusintha!! X2

*#VERSE - 2*

Kodi Siudziwa?
Zamadulira Ndizopweteketsa...
Kuona Maso A nkhono Nkudekha!
Kodi Siudziwa???

Kodi Siudziwa?
Nsabwe Yoyendayenda Inakumana Nacho Chala...
Kodi Siudziwa???

Kodi Siudziwa?
Moyo Sagula Ndi Ndalama...
Moyo Ndi Wodula!
Kodi Siudziwa???

Kodi Siudziwa?
Imfa Ilibe Odii!!
Imadza Ngati Mbala...
Kodi Siudziwa???

Kodi Siudziwa?
Uthenga Uwunyozerawu
Mawa Udzaufuna...
Kodi Siudziwa???

*(Back to Chorus)*

*#BRIDGE*

Oh! Zimatha Kusintha!
Zimatha Kusintha!
Zimatha Kusintha! X 2

(Osanyoza Wena...
Lemekeza Aliyense...
Siudziwa Mawa Libala Chani...
Usadalire Chuma...
Poti Chuma Ndi Mame...
Mawa Libalanji'we?... Limbikira Maphunziro...
Mundinyoza Lero...
Muti Ndine Kape...
Siudziwa Mawa Libalanji'we...)